Phyzix ft Dare Devils – Makofi – Lyrics

0

Intro: GD

Makofi
Let’s roll
I see you talking too much on Social Media man So from now on
Ndizingogawa makofi Ndanyasidwa
Ndizingogawa makofiNdaipidwa
Asamaphweketse GAMBA
Ndizingogawa makofi

Verse 1: Phyzix

Sindikunyengelera mwana wa munthu
ndikugawa makofi minimum ndi two 2
Ngati ndinachalira ndakwiyilatu
Kundiputa ineyo iwe akwililatu
Mafanawa akumamasukatu 
Kunditapa nkamwa kumathoka za mkutu
Ena ndi ma Gangsta pa Facebook
 amachenjela pa zopusa ngati ukuku
Nkhuku ngati iwe kuputa Kambuku?
Kabudula wanji kunyoza buluku?
Ena ndi mafumu ine ndi Gulupu
Musamandichimwitse ndikaika ma Lupu
Very Good! Very Good!

Hook: Phyzix & GD

Mwati bwanji
Ndizingogawa makofi Mabwande
Ndizingogawa makofi
Ala ala ala ala
Asamaphweketse GAMBA Ala ala ala ala
 Ndizingogawa makofiMwati bwanji
Ndizingogawa makofi Mabwande
 Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
 Asamadelere GAMBA Ala ala ala ala
 Ndizingogawa makofi

Verse 2: Marcus

I do it all for love..mufunseni..Sangie
Izi ndiza real izi sizamasanjie
Sindimaimba gospel bwanji??
Dikilani ndiimbe gospel bwanji..
Okay..thank God it’s a friiiiiidaaaaay!!!!
Mmene ulili bwino uli baaadaaay..??
Eh aise nyimboyi ndaiphadiii!!!
Ndikutchinjiriza uku ngati padiiiii
Ndikupatsani makofi
Mamuna saamwa tea amangomenya cofee
Lero muli ziii munkati tinatha!!!
Mufunse Stich Fray… ma devilz amatha!!

Hook: Phyzix & GD

Mwati bwanji/ Ndizingogawa makofi
Mabwande
Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
 Asamaphweketse GAMBA Ala ala ala ala
 Ndizingogawa makofiMwati bwanji
 Ndizingogawa makofiMabwande
Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
 Asamadelere GAMBAAla ala ala ala
 Ndizingogawa makofi

Verse 3: GD

Am not clever with a status
So instead of twitter fingers man am slapping all my haters
Social media never made us
I was made in the streets so when I see you say your prayers
Ana apatchire kupanda mwambo
Vuto losakula ndi bambo
Makani ngati mfiti sangamve opanda jando
Mwakumana ndi savage trumpu saopa Scandal
Ndizingowaza ma Kofi
Kumadzimva suwiti tikutafuna tofi
Kukupatsani bala ndikutsirapo salti
Kumenyedwa pa njira nkumenyedwanso Ku khothi

Hook: Phyzix & GD

Mwati bwanji
Ndizingogawa makofi Mabwande
 Ndizingogawa makofiAla ala ala ala
 Asamaphweketse GAMBAAla ala ala ala
Ndizingogawa makofiMwati bwanji
Ndizingogawa makofiMabwande
Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
Asamadelere GAMBA Ala ala ala ala
Ndizingogawa makofi

Verse 4: Phyzix

Kugawa makofi ngati ku restaurant
Kugawa makofi ngati Office Assistant
Panopo zausilu ndili resistant
Yemwe andipute makofi ndi instant
Ma bars a ineyo ndi a ku Chichiri
Ndinamangilira game ndi momwe ziliri
Mundipeza ndili phee cha pa zinziri
Tima bae m’mbalimu tikungoti katswiri
Why u wanna mess with me
 huh?Is it because am MVP
bruh?Why u wanna mess with me
 huh?Is it because you envy me
 bruh?

Hook: Phyzix & GD

Mwati bwanji
Ndizingogawa makofi Mabwande
Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
Asamaphweketse GAMBA Ala ala ala ala
 Ndizingogawa makofiMwati bwanji
Ndizingogawa makofiMabwande
Ndizingogawa makofi Ala ala ala ala
Asamadelere GAMBAAla ala ala ala
Ndizingogawa makofi

Outro: Phyzix

Am gonna break alotta Twitter fingers this year
Facebook, WhatsApp… anthu mwamasuka kwambiri.
 Gamba. Phyzix

Download Mp3 Here Find out more on our Blog

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More