Verse 1
A Rozi kununkha zithukuta, khungu mu zala kukupuka
magobo kusintha ka move ka, nane ndufuna kutukuka
mwandionela pansi mochuluka, vuto mtima ku susuka
sinfuna zingini zoguluka, ndufuna zonyada nazo kugulu ka
ti tsitsi ti dzala tojuduka, ntchafu, ka mbina kotuluka
skin yako yeni yeni yokuda, osati zochapa zosuluka
uuhh za ife osaulula, tsiku silitha osakutchula
osalephela okukhumula komabe, m’dalitso kumwamba kubhuduka
ah ah mpaka ndikusalile kudya?
huh? ukufuna chani kweni kweni
mpaka ndikumangile nyumba?
huh? international item
mpaka ndikuvaile kunja?
huh? unakapola moto koma
usandisaize thumba
Rose anthu akumva eish
kununkha zithukuta, khungu mu zala kukupuka

Hook
Olo munganyade, olo munganyade
ife timagwila ntchitoooo
ife timagwila , yebo yebo yebo uh huh Ololo
A Rozi munganyade, A Rozimeri munganyade
ife timagwila ntchito, A Rozimeri munganyade
Verse 2
Ine mpaka manyazi, nkhawa zoyambisa danzi
ndikakuona ndi fanzi, phuma kuthamanga mwazi
usandipake u swazi rozi, kundidyesa nazo frasi
kusonkhezela ti ma handz, kuti mwina umweko ti madzi
olo ukupanga zotamika, rozi iwe ndi makina
waziulemu zosefukila, wa zovala zobisa zi mang’ina
i swear chilichonse ungafunecho ndipanga iyo si nkhani ka
pa iwe mutu unaima, kunokola mutu wa scania
takambika, mpaka tikutengele khini?
huh? kuti undilole,
mpaka ndikutemele mphini
huh? sangandisunthe pa iwe
olo akusemele ngini
nde usalole zokamba za anthu
zisinthe the way that you see me
ndinebe katswiri eeh
Hook
Olo munganyade, olo munganyade
ife timagwila ntchitoooo
ife timagwila , yebo yebo yebo uh huh Ololo
A Rozi munganyade, A Rozimeri munganyade
ife timagwila ntchito, A Rozimeri munganyade
Stream and Download the song HERE and visit our Homepage for more