Mbola

0

POST CHORUS
Daily kukhala mmaluzi(mbola)/
Kukhala sober tsiku lonse (mbola)/
Kupanga leak zima nudes (mbola)/
kupopa mbola Chifukwa akudyesa banz! (Mbooola)

VERSE 1
Ndikufuna kuchapa koma madzi sakuyamba/
Ndikufuna ku sita koma magetsi sakuyaka/
Kodi tizikhalira ma blackout?/
Magetsi kuthima throughout?/
Life tiipanga bwanji sort out?/
Zoti muzapanga fix i doubt/
Ati abweretsa chi 4G(mbola)/
Aneba 4.5 (mbola)/
Zonse sizikugwira(mbola),
haa! net ya ku malawi ndi Mbola!

PRE CHORUS
Ngini ndi mbola
Crack akuti beat yi so ndi mbola
a police akuti atimanga nde ndi mbola
Ife timamvetsa kuwawa ngati tsabola

CHORUS
Game yi ndi mboooooola aaaaaaaaah
Game yi ndi mbola
Mbola! Mbola ,mbola
Gist yi ndi mboooooola aaaaaaaah
Gist yi ndi mbola
Mbola! mbola! mbola!

POST CHORUS
Daily kukhala mmaluzi(mbola)/
Kukhala sober tsiku lonse (mbola)/
Kupanga leak zima nudes (mbola)/
kupopa mbola Chifukwa akudyesa banz! (Mbooola)

VERSE 2
Masten ku pheya fees/
Mfana wanga atenge degree/
Four years kutenga degree/
koma nanga ntchito ndiipeza lit?
Aaaaah guys ndingoyamba ma gain?( mbola)/
Koma ma loss again and again (mbola)
Kumalawi tikungomvako pain/
maluz akutibaya ndi mpeni
Kapena ndivaye ku theba?(mbola)/
Ndikangoyamba kuba?(mbola)/
Kapena ndikalowe labour?/
kumalawi tatopa kudya zitheba

PRE CHORUS
Ngini ndi mbola
Crack akuti beat yi so ndi mbola
a police akuti atimanga nde ndi mbola
Ife timamvetsa kuwawa ngati tsabola

CHORUS
Game yi ndi mboooooola aaaaaaaaah
Game yi ndi mbola
Mbola! Mbola ,mbola
Gist yi ndi mboooooola aaaaaaaah
Gist yi ndi mbola
Mbola! mbola! mbola

POST CHORUS
Daily kukhala mmaluzi/
Kukhala sober tsiku lonse /
Kupanga leak zima nudes /
kupopa mbola Chifukwa akudyesa banz!

OUTRO
mbola! mbola! mbola!

POST CHORUS
Daily kukhala mmaluzi(mbola)/
Kukhala sober tsiku lonse (mbola)/
Kupanga leak zima nudes /
kupopa mbola Chifukwa akudyesa banz! (Mbooola)
Ma! ma! mapiri

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More