INTRO
Call me Mr. Story Teller
Am Blakjak,, Indzee!
VERSE ONE
Nnali ndi Show Ku Mwanza, (Kunali bwaaaa?)
Kunadzadza
Nnali ndi Show Ku Balaka, (Watchillaa tu)
Ndinablaka
Nnali ndi Show Ku Mulanje, (Unakoka eti?)
Aaah Njee
Nnali ndi Show Ku Bangwe, Mpaka Mbee
Koma Nkhope Zake Zinali Zomwezo
Akazi ake Anali Omwewo
Zovala zakenso zomwezomwezo
Ndipo Nkhani Zomwe Ankakamba Zinali Zomwezo
Koma Satopa
Akayamba kuvina iwo Safooka
Akalowa Mbwalo Sachoka
Ndipo palibe Anganame kuti shhhh**
HOOK
Akazi Ake Ndi Omwewo Omwewo Omwewo Omwewo
Omwewomwewo
Akazi Ake ndi Omwewo (Iwe Sumadziwa)
Omwewo (Uyisova) Omwewo ×2
VERSE TWO
Dzana Kunabwera Lucius (Abamdulana) Ndi Blaze
Dzulo Anali ndi Shozie, (Amatani) Amayimba Ku Chez
Lero Ati Akupita Ku Mubawa (Kuli Chani) Kuli Nep ndi Makawa
Ku Mkango Lodge Ati Azapita Mawa, Kuli Chani? Kaya
Koma Satopa
Akayamba kuvina iwo Safooka
Akalowa Mbwalo Sachoka
Ndipo palibe Anganame kuti shhhh**
HOOK
VERSE THREE
Dzana Amafuna 2pin, Ndamfaka
Dzulo Amafuna 1pin, Wabwera Wathwala
Lero Ati Akufuna 5 hanzi iii Ndamuuza Mayazi
Basi wayamba Kupanga Screen shot Zijazi, Akuwonetsa Fans
HOOK ×2