Piksy – Umakwana – Lyrics

0

VERSE 1
Osanama iwe wekha umakwana
Kukutobwanya ngati kutobwanya mwana
Thupi kufewa
Kodi mafuta omwewa
Ndiri pa easy ena akuphula njerwa
Ukamachoka mnthupi mwanga mumachema
Ndimakonda kukuyang’ana ngati kanema
Ndipatse nkono uvine ndi angozo
Ma hope akowo uwauze no go zone

CHORUS
Kunditchula sweetie ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Babie umakwana
Kunditchula sweetie ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Dale umakwana

VERSE 2
Ndikumva kukoma andimva madzi chaka chino
Akumva kuwawa akungokhalira cafenol
Mutu kuphwanya akungotuluka kamfuno
Sakumagona akumwa mankhwala a tulo
Wandiloka
Koma apa palibe kuchoka
Wandifoola
Mphamvu zanga apa zikushota
Wandiloka
Koma apa palibe kuchoka
Wandifoola
Mphamvu zanga apa zikushota

CHORUS

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More