Nesnes – Yankho – Lyrics

0

Intro

Nesnes.., Yeah…

Verse 1

Yesu ndimudziwa ine samalephera
Yesu ndimudziwa ine amagonjesa
Master Jesus there is no one like you
Master Jesus palibe ofana naye
Doctor Jesus palibe mthenda yomukanika
Papa Jesus amakonda ana ake onse
Nthawi yamavuto tamuyitane
Nthawi yamavuto call his name

Chorus

Pukuta misozi yako
bwelesa Vuto lako
Kwa Yesu anali yakho (iyeyo)
Alinayo yakho oh oh(iyeyo)
Salephera
Salephera aaah
Salephera
Yesu salephera

Verse 2

Uvutikilanji nyumba mwa bambo
Ako muli chuma ona walemedwa
Bwela kwa Bambo ako zakutula
Khulupilila iye siliva ndi golide zake
Ananesa iye muthawi yamavuto
Timuyitane

Chorus

Pukuta misozi yako
bwelesa Vuto lako
Kwa Yesu anali yakho (iyeyo)
Alinayo yakho oh oh(iyeyo)
Salephera
Salephera aaah
Salephera
Yesu salephera

Bridge

Master Jesus yeah
Doctor Jesus kuchikweza

Chorus X2

Master Jesus
Mfumu Jesus
Master Jesus
Doctor Jesus X2
Zonse Jesus yeah

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More