Mafo – Babie Yanga – Lyrics

0

Intro
Aha madala mafo
Mwini filimu
Madala mafo

 

Chorus
Sitipatsana dolla ndi babie yanga koma. Love yokhayo ayiayiyaa
Sititengelana kumalo odula koma love yokhayo. Ayiyayaayaaa
Sitipatsana dolla ndi babie yanga koma love yokhayo ayiyayaaiyaya
Sititengelana kumalo odula koma love yokhayo ayayayaaa
Zomwe timapatsana ndi hug ndi kiss basi
Mphatso timapatsana inde koma pa khrismasi
Dzana kanabwela kwathu
Dzulo ndinapita kwawo lero tapangana zoti tingokumana pakati
Kakabwera kwathu ndimangoti ente jane ndimadziwa kakudzandipanga entertain
Ndikangakanga akaka ka entertainer
Zoti kanagwa kumwamba ndimatero pena
Ndendikokongolatu mophipirira ndimati pa iyeyo chauta anasinjirira apo ayi
Kukongolako iyeyo anaphangira
Sindimvetsabe ndimmene anampangira
Koma warge dzapatse chani mkaziyu kayatu.
Ndizatani nae ine mkaziyu kayatu ine ine ish warge mkaziyu kayatu hahaaha

 

Chorus
Kamandisowa olo ndikhale kuti ndili nako pomwepo kakangoti darling ndi chi kiss pomwepo
Tikayamba ma game ka mandibongesa nawo
Or miyendo yake kamandibongesa nayo
Mmene ndinkaka chaser ndinali nditayaka
Katati mafo utaye mowa ine nditayaka
Pano zaka 4 zatha tikuzemberana moti teletela apa titengana
Timatengana wakuphiri ine ndi igor tikhale pamtengo ndidzikamenyera nyimbo
Ndikamenya riddle kamaseka mwaphamvu
Pano katupa saya kanalumidwa ndi mavu
Kali crazy heve ndimmene ndukaonera
Ndikakachotsa bra ngati siine ndukaonera
Ndikowala simungagwire inuo acina billiad
Ndukayikaso ngati kamapanga nawo gilliad

 

Chorus
Chomwe timapatsana ndi hug ndi kiss bac mphatso timapatsana inde koma pa khrismas
Dzana kanabwela kwathu dzulo ndinapita kwawo lero tapangana zoti tingokumana pakati kakabwera kwathu ndimangoti enter jane ndimadziwa kakudzandipanga entertain
Ndikangakanga akakaentetainer
Zoti kanagwa kumwamba ndimatero pena
Ndendikokongolatu mopitirira
Ndimati pa iye chauta anasinjirira apo ayi
Kukongolako iyeyo anaphangira sindimvetsabe ndimmene anapangira
Koma warge ndidzampatse chani mkaziyu kayatu
Ndizatani naye mkaziyu kayatu ine ine ish warge mkaziyu kayatu
Chorus

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More