Eli Njuchi – Zitheke – Lyrics

0

INTRO

Up deh we ah fih Inspire de Yuts Dem
Njuchi!!!
Eli!!!
Woyoiiii

(HOOK)

Ndimaphusha Mpaka Zitheke
Phusha Mpaka Zitheke
Bwana Dollar zanga Gwetsaniiii
Zomwezi mpaka Mipeni
Ndimaphusha Mpaka Zitheke
Phusha Mpaka Zitheke
Bwana Dollar zanga Gwetsaniiii
Zomwezi mpaka Mipeni

(VERSE 1)

Eli Njuchi cham’ma one ndine Venda
Cham’ma two ndine Conductor
Past Three ndine Bus driver
Tidutseko bwino zingade bwino uko bwino Magazi udzandipeza Nditasenza Thumba
Ndimete Anthu twenty before Ten Bar
Magetsi akathima sindithera
Sititola Chikwama ase timasoka
Ngati sikuphula Ndidyera Pamoto pompa
Breda am Blessed
Funa Dollar Zidzadze Mu Besenii
Bwana Bwana Dollar zanga gwetsani,Zomwezi mpaka mipeni

(HOOK)

(VERSE 2)

Mumam’va Bwanji
Akati masten agona Ndinjala Chifukwa Chosowa Khusa
Nde Ndamva nkhani
Hustle Ukamayipemphelera sungakwatirane ndi Maluzi
Ndimaphusha mpaka zitheke
Kusaka Link Mpaka Made on Monday timveke
Kudya Books Heavy mawa Jeso iphweke
Zina Invest,Zotsalazo Zidye
Money ah fih Multiply like Pablo
Hustle Clean Clean siza El Chapo
Premier Bet k150 ilowepo
NdimaBetabe Olo ndife ndiimooooo!!

(VERSE 3)

A Eli Njuchi ma Show osewa
Ndamva Zoti dzana Dzulo unali Mbali Ya Dowa
Tikudziwa Musaname Ndalama Zalowa
Nafe Tikufuna (pluu!!) ma Iphone wa
Eeey!
Dem never Know ndili Pachi Budget
Olipah tings are Planned wanna buy a private jet
Nuff ah Dem ah come busy keep me Suffocating
Nthawi sinakwane Yogulira munthu skirt
Breda am Blessed
Funa Dollar zidzadze mu Beseni
Bwana bwana Dollar zanga Gwetsaniiii
Zomwezi mpaka mipenii

(HOOK)

OUTRO

(Yeah!!)

ZITHEKE ZITHEKE !!!
(Oooh!)
ZITHEKE ZITHEKE!!!
(Yeah!)
ZITHEKE ZITHEKE!!!
(Ooooh!!!)
ZITHEKE ZITHEKE!!!
(Yeah!)
ZITHEKE ZITHEKE!!!
(Gwetsa mandede iwe eh eh)
ZITHEKE ZITHEKE !!!!!
(Gwetsa mandede iwe eh eh)

Download the track here and catch more lyrics here

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More