Avokado ft Slessor – Njododa – Lyrics

0

Intro
Pakuti mneneri Paulo ananena kuti ndalimbana nako kwabwino
Avokado ayise
Slessor
Avo
Avo
Avo

Verse 1: Avokado
Eyo Slessor/
Mafanawa ndi matube nkona tikuphwesa/
Ankaziva udolo ona pano anapepera/
Team yathu Phwanga level ya achina Pepe/
Ankapanga phokoso ona pano kulichete/
Flow ya Ine rapper wako ali njenje/
Chimfana chotchuka zoba sungapange mfwemfwe/
Rapper wako uja pano anasiya kumveka/
Tinamuthira loko pakamwa tinatseka/
Lozeleni Ine level ya Ine /
Sinduonapo pano level ya ine/ RA
Lozeleni Ine level ya Ine/
Sinduonapo pano level ya ine/

Chorus
Almhadulilah
Njododaaa
Mafana mwachepa
Njododaaa
Tiyee Wii
Njododaaa
×2

Verse 2: Slessor
I tried to tell em am a top five rapper/
Ankati Slessor top five? Amakhafa/
Mfana wa zisudzo koma jokes sindi trappa/
Mfana wa zi luso koma ngo’ sindikamba/
Ankati Slessor beef sangayikwanitse/
But for me beef is protein nde pa easy/
Billingual flow/ sindineso many more/
Done with touching base pano kwangosala channel O/
Mwiniwake wa beef ndadza ndi Avakado/
Ndili hoti mu streets musamapange mwano/
Ma rapper omwe ndimakhulana nawo/
Onse anasupuka amayesa ndi bawo/
Sindimakhululuka sine mchewali wawo/
pano zavumbuluka tikumana mzigawo/
I wish you knew that I was trouble from a distance/
Ndikaluza beefi I be flexin on ur mistress/
Kudutsa mu n’ganjo koma Moto sunandiphe/
Flow so easy koma awo sinandithe/
Kumapanga zi ngini osamayesa/
Anatemera mphini achina Slessor

Chorus
Almhadulilah
Njododaaa
Mafana mwachepa
Njododaaa
Tiyee Wii
Njododaaa
×2

verse 3: Avo Kado
Achina Ujeni asylum alykum/
Munali kale munayoyoka ngati chigumu/
Tinaononga career yanu Ife ndife mfiti/
Ngati sudziwa Avo kwanu kulibe TV/
Njodo Dada mbape mbape/
Ifeyo ndi madada iwe gwape/
Avokado Slessor legend legend legend/
Level yathu Phwanga ndi mwala wa mulegeni/
Ndinatchuka heavy kuden kwanu konse/
Mumavera Nyimbo zanga osapanga pause/
Industry yopanda Avo music singabebe/
Munkaishosha mumvaBeBe/

Chorus
Almhadulilah
Njododaaa
Mafana mwachepa
Njododaaa
Tiyee Wii
Njododaaa
×2

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More