Jungle Jex – Siza Normal – Lyrics

0

Intro
Nah nah nahyi
Stah tah tahyi
Jungle Jex You know

Hook
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Verse 1
Kulibwino kungouzana kuti chathapo,
Zikafika potele zalowa nthenya//
Ndithu kungouzana band chathapo,
Ngati inali ya 47 yalowa Ngwenya//

Nkhani ya chikondi siyomasewera nayo,
Ma seconds omwewa ena akulira nawo//
Nkhani ya chikondi siyolubwalubwa nayo//
Fusa makolowa mowe akulira nayo//

Nde ukandipatse ineyo tchuthi//
Kuyembekezera dovuno chuchi//
Nde ukandipatse ineyo break//
Pomwe ali mathero awa beib//

Hook
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Verse 2
Pakakhalatu pa school pa break pompo//
Mwana wa school amatha kuthawira//
Pakakhalatu pa school pa holiday po//
Mwana wa school amatha kutenga mimba//

Kodi ukuti chani za holiday iwe//
Ndi chimodzimodzi mkazi ulibe iwe//
Ndipo ukuti chani za break iyo//
Ndi chimodzimodzi heart break iyo//

Nde ukandipatse ineyo tchuthi//
Kuyembekezera dovuno chuchi//
Nde ukandipatse ineyo break pomwe ali mathero awa beib//

Hook
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Verse 3
Ngakhale kumufusa openga//
Ayankha iyeyo aope nda//
Ndikuti kumufusa wamisala//
Akuuza break yo nde misala//

Chibwenzi zamapumila Kaye//
Akangonena chomcho iwe umutaye//
Chibwenzi sichikhala ndi tchuthi//
Akatero dziwa wakulumitsa njuchi//

Chibwenzi sichikhala ndi tchuthi//
Noh Noh Noh Noh Noh Noh//
Chibwezi sichikhala ndi holiday//
Noh Noh Noh Noh Noh Noh//

Kulibwino kungouzana kuti chathapo//
Zikafika potele zalowa nthenya//
Ndithu kungouzana band yathapo//
Ngati inali ya 47 yalowa ngwenya//

Nde ukandipatse ineyo tchuthi//
Kuyembekezera dovuno chuchi//
Nde ukandipatse ineyo break//
Pomwe ali mathero awa beib//

Hook
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine Sizanormal,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday//

Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi break//
Kwa ine sizonveka,
Chibwenzi anzanga kukhala ndi holiday/

Leave a Reply

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More