Verse 1
Hun Pomwe Mwakhalapa pompa apa /
Analipo Ena Anka Dzipopa Apa /
Ankandiuza Sadzandisiya /
Ankati Ndine ndekha amafila /
Eh Nawonso Anka Lonjeza /
Kuti Sadza Longedza /
Anasintha Mawanga /
Kundiswera Mtima wanga
Pre – Hook
Anandipekera Dzinkhani /
Kundionongera plan /
Ndeno Undiudza Chani ? /
Pereka Manifesto
Hook
Kodi Suli Ngati Enawa? /
Suli Ngati Enawa? /
Sudzandi Thawa Chikondi Chikukoma baybay. . X2
Verse 2
Nde Nde Nde, Zimene mukunena /
Anandiuzaponso Ena /
No me No Life /
No me No life /
Pano Alimoyo /
Anawa namiza awo..Anasintha Mawanga /
Kundiswera Mtima wanga
Pre – Hook
Anandipekera Dzinkhani /
Kundionongera plan /
Ndeno Undiudza Chani ? /
Pereka Manifesto /
Hook
Kodi Suli Ngati Enawa? /
Suli Ngati Enawa? /
Sudzandi Thawa Chikondi Chikukoma baybay. . X2
Bridge
Ndifuna Kudziwa /
Ngati Chikondi Chako Chimapanga Expire /
Ndati Undiuze Iweo /
Suzanditaya? Ndili Ndi Mantha Ineyo /
Ndi Mantha Ineyo /
Sindizadzipha Ineyo? .. Nanana